Salimo 76:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu mumawala kwambiri.*Ndinu waulemerero kuposa mapiri amene muli nyama zodya zinzake.