Salimo 77:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa tsiku limene ndakumana ndi mavuto ndimafunafuna Yehova.+ Usiku ndimakweza manja anga kwa iye ndipo sindisiya.* Palibe chimene chimanditonthoza.
2 Pa tsiku limene ndakumana ndi mavuto ndimafunafuna Yehova.+ Usiku ndimakweza manja anga kwa iye ndipo sindisiya.* Palibe chimene chimanditonthoza.