-
Salimo 77:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kodi chikondi chake chokhulupirika chatha mpaka kalekale?
Kodi malonjezo ake sadzakwaniritsidwa ku mibadwomibadwo?
-