Salimo 77:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Mulungu, njira zanu ndi zoyera. Kodi pali mulungu winanso wamkulu amene angafanane ndi inu Mulungu?+
13 Inu Mulungu, njira zanu ndi zoyera. Kodi pali mulungu winanso wamkulu amene angafanane ndi inu Mulungu?+