Salimo 77:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndi mphamvu zanu* mwapulumutsa* anthu anu,+Ana aamuna a Yakobo ndi a Yosefe. (Selah)