Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu+ linali ngati la mawilo a galeta.Kungʼanima kwa mphezi kunaunika padziko lapansi.+Dziko lapansi linanjenjemera komanso kugwedezeka.+
18 Phokoso la bingu lanu+ linali ngati la mawilo a galeta.Kungʼanima kwa mphezi kunaunika padziko lapansi.+Dziko lapansi linanjenjemera komanso kugwedezeka.+