Salimo 78:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,Ndipo anaika chilamulo mu Isiraeli.Iye analamula makolo athuKuti auze ana awo zinthu zimenezi,+
5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,Ndipo anaika chilamulo mu Isiraeli.Iye analamula makolo athuKuti auze ana awo zinthu zimenezi,+