Salimo 78:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anayesa Mulungu mʼmitima yawo+Pomuumiriza kuti awapatse chakudya chimene ankalakalaka.