Salimo 78:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho iwo analankhula mawu amwano kwa MulunguKuti: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya mʼchipululu muno?”+
19 Choncho iwo analankhula mawu amwano kwa MulunguKuti: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya mʼchipululu muno?”+