Salimo 78:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.Anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 78:24 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 11