Salimo 78:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iye ankakumbukira kuti iwo ndi anthu athupi la nyama,+Ali ngati mphepo imene imadutsa ndipo sibwereranso.*
39 Iye ankakumbukira kuti iwo ndi anthu athupi la nyama,+Ali ngati mphepo imene imadutsa ndipo sibwereranso.*