Salimo 78:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Anapha nyama zawo zonyamula katundu pogwiritsa ntchito matalala,+Ndiponso ziweto zawo ndi mphezi.