-
Salimo 78:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,
Komanso ukali wake ndipo anawabweretsera mavuto,
Anawatumizira magulu a angelo kuti awabweretsere tsoka.
-