Salimo 78:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mkwiyo wake anaulambulira njira. Sanawapulumutse ku imfa,Ndipo anawagwetsera mliri.*