Salimo 78:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka mʼmatenti a Hamu.
51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka mʼmatenti a Hamu.