Salimo 78:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Iwo anasiyanso Mulungu ndipo ankachita zinthu mwachinyengo ngati makolo awo.+ Anali osadalirika ngati uta wosakunga kwambiri.+
57 Iwo anasiyanso Mulungu ndipo ankachita zinthu mwachinyengo ngati makolo awo.+ Anali osadalirika ngati uta wosakunga kwambiri.+