Salimo 79:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+ Tisonyezeni chifundo chanu mofulumira,+Chifukwa zativuta kwambiri.
8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+ Tisonyezeni chifundo chanu mofulumira,+Chifukwa zativuta kwambiri.