Salimo 79:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+ Anthu a mitundu ina adziwe ife tikuonaKuti mwabwezera magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa.+
10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+ Anthu a mitundu ina adziwe ife tikuonaKuti mwabwezera magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa.+