Salimo 79:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Imvani kuusa moyo kwa mkaidi.+ Gwiritsani ntchito mphamvu zanu zazikulu* kupulumutsa anthu amene aweruzidwa kuti aphedwe.*+
11 Imvani kuusa moyo kwa mkaidi.+ Gwiritsani ntchito mphamvu zanu zazikulu* kupulumutsa anthu amene aweruzidwa kuti aphedwe.*+