Salimo 79:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mukatero, ife anthu anu komanso nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Ndipo tidzalengeza kuti inu ndi woyenera kutamandidwa ku mibadwomibadwo.+
13 Mukatero, ife anthu anu komanso nkhosa zimene mukuweta,+Tidzakuyamikani mpaka kalekale.Ndipo tidzalengeza kuti inu ndi woyenera kutamandidwa ku mibadwomibadwo.+