Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+ Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+Onetsani kuwala kwanu.*
80 Inu Mʼbusa wa Isiraeli, mvetserani,Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+ Inu amene mwakhala pampando wachifumu pamwamba* pa akerubi,+Onetsani kuwala kwanu.*