Salimo 81:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 Fuulani mosangalala kwa Mulungu amene ndi mphamvu yathu.+ Fuulirani Mulungu wa Yakobo mosangalala chifukwa wapambana.
81 Fuulani mosangalala kwa Mulungu amene ndi mphamvu yathu.+ Fuulirani Mulungu wa Yakobo mosangalala chifukwa wapambana.