Salimo 81:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ndinachotsa katundu wolemera paphewa lake.+Manja ake anamasuka moti sankanyamulanso dengu.