Salimo 83:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muwathamangitse ndi mphepo yanu yamphamvu,+Ndipo muwaopseze ndi mphepo yanu yamkuntho.+