Salimo 84:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akamadutsa mʼchigwa cha Baka,*Amasandutsa chigwacho kukhala malo opezeka akasupe.Ndipo mvula yoyambirira imabweretsa madalitso mʼchigwacho. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 84:6 Nsanja ya Olonda,3/15/1997, tsa. 8
6 Akamadutsa mʼchigwa cha Baka,*Amasandutsa chigwacho kukhala malo opezeka akasupe.Ndipo mvula yoyambirira imabweretsa madalitso mʼchigwacho.