Salimo 84:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima nʼkutipatsa ulemerero. Yehova sadzalephera kupereka chinthu chilichonse chabwinoKwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 84:11 Nsanja ya Olonda,5/1/2009, tsa. 14
11 Chifukwa Yehova Mulungu ndi dzuwa+ ndiponso chishango.+Iye amatikomera mtima nʼkutipatsa ulemerero. Yehova sadzalephera kupereka chinthu chilichonse chabwinoKwa anthu amene amachita zinthu mokhulupirika.+