Salimo 86:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tetezani moyo wanga chifukwa ndine wokhulupirika.+ Pulumutsani mtumiki wanu amene amakukhulupirirani,Chifukwa ndinu Mulungu wanga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:2 Nsanja ya Olonda,12/15/1992, tsa. 9
2 Tetezani moyo wanga chifukwa ndine wokhulupirika.+ Pulumutsani mtumiki wanu amene amakukhulupirirani,Chifukwa ndinu Mulungu wanga.+