Salimo 86:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma inu Yehova, ndinu Mulungu wachifundo komanso wokoma mtima,Wosakwiya msanga, wachikondi chokhulupirika chochuluka ndiponso wokhulupirika.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:15 Nsanja ya Olonda,12/15/1992, tsa. 17
15 Koma inu Yehova, ndinu Mulungu wachifundo komanso wokoma mtima,Wosakwiya msanga, wachikondi chokhulupirika chochuluka ndiponso wokhulupirika.*+