Salimo 86:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndisonyezeni chizindikiro cha* ubwino wanu,Kuti anthu amene amadana nane aone ndipo achititsidwe manyazi, Chifukwa inu Yehova ndi amene mumandithandiza komanso kundilimbikitsa. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:17 Nsanja ya Olonda,4/15/1993, tsa. 3112/15/1992, ptsa. 17-19
17 Ndisonyezeni chizindikiro cha* ubwino wanu,Kuti anthu amene amadana nane aone ndipo achititsidwe manyazi, Chifukwa inu Yehova ndi amene mumandithandiza komanso kundilimbikitsa.