-
Salimo 87:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ponena za Ziyoni anthu adzati:
“Aliyense anabadwira mmenemo.”
Ndipo Wamʼmwambamwamba adzakhazikitsa mzinda umenewo ndi kuulimbitsa.
-