Salimo 88:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ine ndimafuulirabe kwa inu Yehova kuti mundithandize,+Mʼmawa uliwonse pemphero langa limafika kwa inu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 88:13 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, ptsa. 14-15
13 Koma ine ndimafuulirabe kwa inu Yehova kuti mundithandize,+Mʼmawa uliwonse pemphero langa limafika kwa inu.+