Salimo 88:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyambira ndili mnyamata,Ndakhala ndikuzunzika komanso kutsala pangʼono kufa.+Ndafooka kwambiri chifukwa cha zinthu zoopsa zimene mwalola kuti ndikumane nazo.
15 Kuyambira ndili mnyamata,Ndakhala ndikuzunzika komanso kutsala pangʼono kufa.+Ndafooka kwambiri chifukwa cha zinthu zoopsa zimene mwalola kuti ndikumane nazo.