-
Salimo 89:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
89 Ndidzaimba mpaka kalekale za mmene Yehova wasonyezera chikondi chake chokhulupirika.
Ndidzalengeza ndi pakamwa panga za kukhulupirika kwanu ku mibadwo yonse.
-