Salimo 89:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Ndidzachititsa kuti mbadwa* zako zikhalepo mpaka kalekale,+Ndipo ndidzachititsa kuti ufumu* wako ukhalepo ku mibadwo yonse.’”+ (Selah)
4 ‘Ndidzachititsa kuti mbadwa* zako zikhalepo mpaka kalekale,+Ndipo ndidzachititsa kuti ufumu* wako ukhalepo ku mibadwo yonse.’”+ (Selah)