Salimo 89:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nyanja ikadzaza mumailamulira.+Mafunde ake akawinduka, inuyo mumawachititsa kuti akhale bata.+