Salimo 89:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzapitiriza kumusonyeza chikondi changa chokhulupirika mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+
28 Ndidzapitiriza kumusonyeza chikondi changa chokhulupirika mpaka kalekale,+Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+