Salimo 89:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ana ake akadzasiya chilamulo changa,Ndipo akadzaleka kutsatira zigamulo* zanga,