Salimo 89:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma inu mwataya wodzozedwa wanu ndipo mwamukana,+Komanso mwamukwiyira kwambiri.