Salimo 89:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mwagwetsa mipanda yake yonse yamiyala.*Mizinda yake ya mipanda yolimba mwaisandutsa mabwinja.