Salimo 89:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kumbukirani kuti moyo wanga ndi waufupi.+ Kodi anthu munawalenga popanda cholinga?