Salimo 89:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kodi pali munthu aliyense amene angapitirize kukhala ndi moyo ndipo sadzafa?+ Kodi angathe kupulumutsa moyo wake ku mphamvu ya Manda?* (Selah)
48 Kodi pali munthu aliyense amene angapitirize kukhala ndi moyo ndipo sadzafa?+ Kodi angathe kupulumutsa moyo wake ku mphamvu ya Manda?* (Selah)