Salimo 90:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi ndani angadziwe kuchuluka kwa mphamvu za mkwiyo wanu? Ukali wanu ndi waukulu mofanana ndi mantha amene tikuyenera kukusonyezani.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 90:11 Nsanja ya Olonda,11/15/2001, tsa. 13
11 Ndi ndani angadziwe kuchuluka kwa mphamvu za mkwiyo wanu? Ukali wanu ndi waukulu mofanana ndi mantha amene tikuyenera kukusonyezani.+