Salimo 90:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mʼmawa, muzitisonyeza chikondi chanu chokhulupirika,+Kuti tizifuula mokondwera komanso kukhala mosangalala+ masiku onse a moyo wathu. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 90:14 Nsanja ya Olonda,11/15/2001, ptsa. 13-14
14 Mʼmawa, muzitisonyeza chikondi chanu chokhulupirika,+Kuti tizifuula mokondwera komanso kukhala mosangalala+ masiku onse a moyo wathu.