Salimo 90:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tichititseni kuti tisangalale kwa masiku ofanana ndi masiku amene mwatisautsa,+Kwa zaka zofanana ndi zaka zimene takumana ndi masoka.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 90:15 Nsanja ya Olonda,11/15/2001, tsa. 14
15 Tichititseni kuti tisangalale kwa masiku ofanana ndi masiku amene mwatisautsa,+Kwa zaka zofanana ndi zaka zimene takumana ndi masoka.+