-
Salimo 91:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Sudzaopa mliri umene umafalikira mumdima,
Kapena chiwonongeko chimene chimachitika masana.