-
Salimo 93:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Inu Yehova, mitsinje yasefukira,
Mitsinje yasefukira ndipo ikuchita mkokomo.
Mitsinje ikupitiriza kusefukira komanso kuchita mkokomo.
-