Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu!
94 Inu Yehova, Mulungu amene amabwezera anthu oipa,+Inu Mulungu amene amabwezera anthu oipa, onetsani kuwala kwanu!