Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 94:18 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 8
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+