Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani, tiyeni tifuule kwa Yehova mosangalala! Tiyeni tifuule mosangalala ndipo titamande Thanthwe la chipulumutso chathu.+
95 Bwerani, tiyeni tifuule kwa Yehova mosangalala! Tiyeni tifuule mosangalala ndipo titamande Thanthwe la chipulumutso chathu.+