Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani, tiyeni timulambire komanso kumugwadira.Tiyeni tigwade pamaso pa Yehova amene anatipanga.+